1 Kings 7:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo pamwamba pake panalinso miyala yabwino kwambiri yosemedwa potsata miyeso yake yofunika, ndiponso pamwamba pa miyalayo panali matabwa amkungudza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pamwamba pake panali miyala ya mtengo wapatali, ndiyo miyala yosemasema monga muyeso wake, ndi mitengo yamkungudza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamwamba pake panali pa miyala yabwino kwambiri, yosemedwa potengera miyeso yake. Pamwamba pa miyalayo panali matabwa a mkungudza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pamwamba pace panali miyala ya mtengo wapatali, ndiyo miyala yosemasema monga muyeso wace, ndi mitengo yamkungudza.