1 Kings 7:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumu Solomoni adatumiza mau ku Tiro kukaitana Huramu kuti abwere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu Solomoni anatuma anthu kukatenga Hiramu ku Tiro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu Solomoni anatuma anthu ku Turo ndipo anakabwera ndi Hiramu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu Solomo anatuma anthu kukatenga Hiramu ku Turo.