1 Kings 7:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adapanga maukonde aŵiri olukanalukana ndi oyangayanga, naŵaika pa mitu ya pa nsanamirazo. Ukonde umodzi pa mutu wina, ndiponso ukonde umodzi pa mutu winanso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali maukonde olukaluka ndi zoyangayanga, zokolana za pa mitu imene inali pamwamba pa nsanamira; zisanu ndi ziwiri za pa mutu wina, ndi zisanu ndi ziwiri za pa mutu unzake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa mitu ya pa nsanamirazo anakolekapo maunyolo awiri olukanalukana ndi oyangayanga. Mutu uliwonse unali ndi maunyolo oterewa asanu ndi awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali maukonde olukaluka ndi zoyangayanga, zokolana za pa mitu imene inali pamwamba pa nsanamira; zisanu ndi ziwiri za pa mutu wina, ndi zisanu ndi ziwiri za pa mutu unzace.