1 Kings 7:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaika nsanamirazo patsogolo pa khonde loloŵera ku Nyumba ya Chauta, ina chakumwera, imene adaitchula Yakini, ndipo ina chakumpoto, imene adaitchula Bowazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaimiritsa nsanamirazi pa chipinda cholowera cha Kachisi; naimiritsa nsanamira ya ku dzanja lamanja, natcha dzina lake Yakini; naimiritsa nsanamira yakumanzere, natcha dzina lake Bowazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anayimika nsanamirazo pa khonde la Nyumba ya Mulungu. Nsanamira ya kumpoto anayitcha Yakini ndipo ya kummwera anayitcha Bowazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaimiritsa nsanamirazi pa likole la Kacisi; naimiritsa nsanamira ya ku dzanja lamanja, nacha dzina lace Yakini; naimiritsa nsanamira yakumanzere, nacha dzina lace Boazi.