1 Kings 7:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pamwamba pa nsanamira zija adakongoletsapo ndi zosemasema zooneka ngati maluŵa a kakombo. Motero ntchito ya nsanamirazo idamalizika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamwamba pa nsanamirazo panali ngati akakombo malembedwe ake; motero anaitsiriza ntchito ya nsanamirazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mitu ya pamwamba pa nsanamirazo inali yooneka ngati maluwa okongola kwambiri. Motero anamaliza ntchito ya nsanamirazo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamwamba pa nsanamirazo panali ngati akakombo malembedwe ace; motero anaitsiriza nchito ya nsanamirazo.