1 Kings 7:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamwamba pa mitandapo panali matabwa amkungudza okuta zipinda zimene zidaamangidwa pa nsanamira 45, pa mzere uliwonse nsanamira khumi ndi zisanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo inayalidwa ndi mkungudza pamwamba pa zipinda makumi anai mphambu zisanu zolongosoledwa pa mapanda, mzere umodzi zipinda khumi mphambu asanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamwamba pa mitandapo panali matabwa a mkungudza amene anaphimba zipinda zimene zinamangidwa pa nsanamira 45, pa mzere uliwonse nsanamira 15.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo inayalidwa ndi mkungudza pamwamba pa zipinda makumi anai mphambu zisanu zolongosoledwa pa mapanda, mzere umodzi zipinda khumi mphambu asanu.