1 Kings 7:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pansi pa matabwawo panali mikombero inai. Tsono mitanda ya mikomberoyo adapangira kumodzi ndi maphakawo. Msinkhu wa mikomberoyo unali masentimita 66.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo njinga zinai zinali pansi pa matsekerezo, ndi mitanda ya njinga inali m'mphakamo, ndi msinkhu wa njinga imodzi unali mkono umodzi ndi nusu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pansi pa matabwawo panali mikombero inayi, ndipo mitanda ya mikomberoyo inalumikizidwa ku phakalo. Msinkhu wa mkombero uliwonse unali masentimita 66.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo njinga zinai zinali pansi pa matsekerezo, ndi mitanda ya njinga inali m'mphakamo, ndi msinkhu wa njinga imodzi unali mkono umodzi ndi nusu.