1 Kings 7:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Phaka lililonse linali ndi zigwiriro zinai, chigwiriro chimodzi pa ngodya iliyonse. Zigwirirozo zidapangidwira kumodzi ndi maphakawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali ngati mapewa anai pansi pangodya zinali za phaka limodzi, mapewawo anali a phaka lomwelo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Phaka lililonse linali ndi zogwirira zinayi; chogwirira chimodzi pa ngodya iliyonse, zolumikizidwa ku phakalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali ngati mapewa anai pansi pa ngondya zinai za phaka limodzi, mapewawo anali a phaka lomwelo.