1 Kings 7:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamwamba pa phaka panali mkombero, msinkhu wake masentimita 22. Tsono pamwamba pa phakalo panalinso zogwiriziza zake ndi matabwa ake, zonsezo zinali zopangidwira kumodzi ndi phakalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamwamba pa phaka panali khoma lozunguniza, msinkhu wake nusu ya mkono; ndi pamwamba pa phaka panali mbano zake ndi matsekerezo a phaka lomwelo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamwamba pa phakalo panali mkombero wozungulira ndipo msinkhu wake unali masentimita 22. Pamwamba pa phakalo panali zogwiriziza ndi matabwa ake, zolumikizidwa ku phakalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamwamba pa phaka panali khoma lozunguniza, msinkhu wace nusu ya mkono; ndi pamwamba pa phaka panali mbano zace ndi matsekerezo a phaka lomwelo.