1 Kings 7:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maphaka khumi aja adaŵapanga motero. Onsewo adapangidwa mofanana, chifukwa miyeso yake inali yolingana ndipo maonekedwe ake analinso ofanana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Motero anapanga maphaka khumiwo, anafanana mayengedwe ao muyeso wao ndi maonekedwe ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Umu ndi mmene anapangira maphaka khumiwo. Onse anawapanga malo ofanana ndipo anali a miyeso yofanana ndiponso wooneka mofanana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Motero anapanga maphaka khumiwo, anafanana mayengedwe ao muyeso wao ndi maonekedwe ao.