1 Kings 7:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndiye kuti kumanga nsanamira ziŵiri zija, kupanga ziwaya zokutira nsonga za makapotolosi okhala pamwamba pa nsanamirazo, ndiponso maukonde aŵiri aja ophimba ziwaya ziŵiri zija za kunsonga kw makapotolosi okhala pamwamba pa nsanamirazo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nsanamira ziwirizo, ndi mbale za mitu inali pamwamba pa nsanamira ziwirizo, ndi maukonde awiri ophimbira mbale ziwiri za mitu inali pamwamba pa nsanamirazo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nsanamira ziwiri; mbale ziwiri za mitu yapamwamba pa nsanamirazo; maukonde awiri okongoletsera mbale ziwiri za mitu yapamwamba pa nsanamirazo;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nsanamira ziwirizo, ndi mbale za mitu inali pamwamba pa nsanamira ziwirizo, ndi maukonde awiri ophimbira mbale ziwiri za mitu inali pamwamba pa nsanamirazo,