1 Kings 7:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiponso adatsiriza maphaka khumi ndi mbiya khumi zija zokhala pa maphakawo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi maphaka khumiwo ndi mbiya khumi zili pa maphakawo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
maphaka khumi pamodzi ndi mabeseni khumi pa maphakawo;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi maphaka khumiwo ndi mbiya khumi ziri pa maphakawo,