1 Kings 7:48 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Solomoni adapangitsanso ziŵiya zimene zinali m'Nyumba ya Chauta: ndiye kuti guwa lagolide, tebulo lagolide la buledi woperekedwa kwa Mulungu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Solomoni anapanga zipangizo zonse za m'nyumba ya Yehova: guwa la nsembe lagolide, ndi gome lagolide loikapo mikate yoonekera;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Solomoni anapanganso ziwiya zonse zimene zinali mʼNyumba ya Yehova: guwa lansembe lagolide; tebulo lagolide pamene ankayikapo buledi woperekedwa kwa Mulungu;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Solomo anapanga zipangizo zonse za m'nyumba ya Mulungu: guwa la nsembe lagolidi, ndi gome lagolidi loikapo mikate yoonekera;