1 Kings 8:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe si ndiwe udzamange nyumbayo, koma mwana wako amene udzabale, ndiye amene adzandimangire nyumba yomveketsa dzina langa.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma usamange ndiwe nyumbayo, koma mwana wako adzatuluka m'chuuno mwako, iyeyo adzamangira dzina langa nyumba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komatu, si iwe amene udzamanga Nyumba ya Mulungu, koma mwana wako, mwana amene iwe udzabereke. Iyeyo ndiye adzandimangire Nyumba.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma usamange ndiwe nyumbayo, koma mwana wako adzaturuka m'cuuno mwako, iyeyo adzamangira dzina langa nyumba.