1 Kings 8:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono m'menemo ndalikonzera malo Bokosi lija, m'mene muli mau a chipangano cha Chauta chimene adachita ndi makolo athu, pamene adaŵatulutsa ku Ejipito.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndakonzera malo likasalo, m'mene muli chipangano cha Yehova, chimene anapangana ndi makolo athu pamene anawatulutsa m'dziko la Ejipito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndalikonzera malo Bokosi la Chipangano mmene muli pangano la Yehova limene anapangana ndi makolo athu pamene anawatulutsa mʼdziko la Igupto.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndakonzera malo likasalo, m'mene muli cipangano ca Yehova, cimene anapangana ndi makolo athu pamene anawaturutsa m'dziko la Aigupto.