1 Kings 8:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Solomoni adaimirira patsogolo pa guwa la Chauta, msonkhano wonse wa Aisraele ukuwona, ndipo adakweza manja ake kumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Solomoni anaimirira ku guwa la nsembe la Yehova pamaso pa msonkhano wonse wa Israele, natambasulira manja ake kumwamba, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Solomoni anayimirira patsogolo pa guwa lansembe la Yehova pamaso pa gulu lonse la Aisraeli ndipo anakweza manja ake kumwamba,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Solomo anaimirira ku guwa la nsembe la Yehova pamaso pa msonkhano wonse wa Israyeli, natambasulira manja ace kumwamba, nati,