1 Kings 8:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mwachitadi zimene mudaauza Davide bambo wanga, mtumiki wanu. Zimene zija mudaalankhula ndi pakamwa panu, dzanja lanu lazichitadi monga onse akuwoneramu lero lino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wakusungira mtumiki wanu Davide atate wanga chimene mudamlonjezacho; munalankhulanso m'kamwa mwanu ndi kukwaniritsa ndi dzanja lanu monga lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwasunga lonjezo lanu kwa abambo anga Davide, mtumiki wanu. Inde zimene munalonjeza ndi pakamwa panu, mwazikwaniritsa ndi manja anu, monga mmene tikuonera lero lino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wakusungira mtumild wanu Davide atate wanga cimene mudamlonjezaco; munalankhulanso m'kamwa mwanu ndi kukwaniritsa ndi dzanja lanu monga lero lino.