1 Kings 8:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usana ndi usiku maso anu azikhala otsekuka kuyang'ana Nyumba imeneyi, malo amene Inu mudanena kuti, ‘Dzina langa lidzamveka m'menemo.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti maso anu atsegukire nyumba yino usiku ndi usana, kumalo kumene munanenako, Dzina langa lidzakhala komweko; kuti mumvere pemphero limene adzapemphera kapolo wanu lolunjika kumalo kuno.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maso anu azikhala otsekuka kuyangʼana Nyumba ino usiku ndi usana, malo ano amene Inu munanena kuti, ‘Dzina langa lidzakhala mʼmenemo,’ choncho imvani pemphero limene mtumiki wanu akupemphera akuyangʼana malo ano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti maso anu atsegukire nyumba yino usiku ndi usana, kumalo kumene munanenako, Dzina langa lidzakhala komweko; kuti mumvere pemphero limene adzapemphera kapolo wanu lolunjika kumalo kuno.