1 Kings 8:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsono munthu akachimwira mnzake, nauzidwa kuti alumbire, akabwera kudzalumbira patsogolo pa guwa lanu m'Nyumba muno,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati munthu akachimwira mnzake, ndi lumbiro likaikidwa pa iye kumlumbiritsa, ndipo akadzalumbira patsogolo pa guwa la nsembe lanu m'nyumba yino;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Munthu akalakwira mnzake, nawuzidwa kuti alumbire, akabwera kudzalumbira patsogolo pa guwa lansembe la Nyumba ino,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati munthu akacimwira mnzace, ndi lumbiro likaikidwa pa iye kumlumbiritsa, ndipo akadzalumbira patsogolo pa guwa la nsembe lanu m'nyumba yino;