1 Kings 8:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kumwamba kukatsekeka, mvula nkupanda kugwa chifukwa chakuti anthuwo adakuchimwirani, pambuyo pake nkupemphera choyang'ana ku malo ano ndi kutamanda dzina lanu, natembenuka nkusiya tchimo laolo Inu mukuŵazunza,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene kumwamba kwatsekera, ndipo kulibe mvula chifukwa cha kuchimwira Inu, nakapemphera iwo molunjika kumalo kuno, ndi kuvomereza dzina lanu, ndi kutembenuka kusiya zoipa zao, pakuwasautsa Inu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pamene kumwamba kwatsekeka ndipo mvula sikugwa chifukwa anthu anu akuchimwirani, ndipo pamene apemphera akuyangʼana malo ano ndi kuvomereza Dzina lanu, ndi kutembenuka kuchoka ku machimo awo chifukwa inu mwawalanga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene kumwamba kwatsekeka, ndipo kulibe mvula cifukwa ca kucimwira Inu, nakapemphera iwo molunjika kumalo kuno, ndi kubvomereza dzina lanu, ndi kutembenuka kusiya zoipa zao, pakuwasautsa Inu;