1 Kings 8:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero anthu anu Aisraele azikuwopani masiku onse a moyo wao, pomakhala m'dziko limene Inu mudapatsa makolo athu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti aope Inu masiku onse akukhala iwowo m'dziko limene Inu munapatsa makolo ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
motero iwo adzakuopani masiku onse amene adzakhale mʼdziko limene munalipereka kwa makolo athu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti aope Inu masiku onse akukhala iwowo m'dziko limene Inu munapatsa makolo ao.