1 Kings 8:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Chimodzimodzinso mwina mlendo amene sali mmodzi wa Aisraele anthu anu, adzabwera kuchokera ku dziko lakutali atamva za dzina lanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiponso kunena za mlendo, wosati wa anthu anu Aisraele, koma wakufumira m'dziko lakutali chifukwa cha dzina lanu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndipo kunena za mlendo amene si mmodzi wa anthu anu Aisraeli, koma wabwera kuchokera ku dziko lakutali chifukwa cha dzina lanu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiponso kunena za mlendo, wosati wa anthu anu Aisrayeli, koma wakufumira m'dziko lakutali cifukwa ca dzina lanu,