1 Kings 8:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi anthu adzamva ndithu za dzina lanu lotchuka ndiponso za dzanja lanu lamphamvu ndi lochita zazikulu. Iyeyo akabwera kudzapemphera ku Nyumba ino,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
popeza adzamva za dzina lanu lalikulu ndi dzanja lanu lamphamvu ndi mkono wanu wotambasuka; akabwera iyeyo nadzapemphera molunjika kunyumba yino;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti anthu adzamva za dzina lanu lotchukali ndiponso za dzanja lanu lamphamvu ndi lochita zazikulu, kudzapemphera akuyangʼana Nyumba ino,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
popeza adzamva za dzina lanu lalikuru ndi dzanja lanu lamphamvu ndi mkono wanu wotambasuka; akabwera iyeyo nadzapemphera molunjika ku nyumba yino;