1 Kings 8:44 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Anthu anu akamapita ku nkhondo kukamenyana ndi adani ao, kulikonse kumene mungaŵatume, akapemphera kwa Inu Chauta choyang'ana ku mzinda umene Inu mudausankha ndiponso ku Nyumba imene ndakumangiraniyi, yomveketsa dzina lanu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akatuluka anthu anu kukayambana nkhondo ndi adani ao, kumene konse Inu mudzawatuma, ndipo akapemphera kwa Yehova molunjika kumudzi uno munausankha Inu, ndi kunyumba ndamangira dzina lanu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pamene anthu anu apita ku nkhondo kukamenyana ndi adani awo, kulikonse kumene mungawatume, ndipo pamene apemphera kwa Yehova moyangʼana mzinda umene mwausankha ndi Nyumba imene ine ndamangira Dzina lanu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akaturuka anthu anu kukayambana nkhondo ndi adani ao, kumene konse inu mudzawatuma, ndipo akapemphera kwa Yehova molunjika ku mudzi uno munausankha Inu, ndi ku nyumba ndamangira dzina lanu;