1 Kings 8:51 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakutitu iwoŵa ndi anthu anuanu ndi choloŵa chanu, omwe aja mudaŵatulutsa ku Ejipito kuŵachotsa m'ng'anjo ya moto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti awa ndi anthu anu ndithu, ndi cholowa chanu chimene munatulutsa m'Ejipito, m'kati mwa ng'anjo ya chitsulo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
popeza ndi anthu anu ndiponso cholowa chanu, anthu omwe munawatulutsa ku Igupto, kuwachotsa mʼngʼanjo yamoto yosungunula zitsulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti awa ndi anthu anu ndithu, ndi colowa canu cimene munaturutsa m'Aigupto, m'kati mwa ng'anjo ya citsulo;