1 Kings 8:52 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Yang'anani mwa chikondi chanu anthu anu Aisraele pamodzi ndi mfumu yao, ndipo muzitchera khutu nthaŵi zonse pamene akupemphani kuti muŵathandize.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti maso anu akatsegukire pembedzero la kapolo wanu ndi pembedzero la anthu anu Aisraele, kuwamvera m'mene monse akafuula kwa Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Maso anu atsekuke kuti aone dandawulo la mtumiki wanu ndiponso madandawulo a anthu anu Aisraeli, ndipo mutchere khutu nthawi iliyonse pamene akulirirani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti maso anu akatsegukire pembedzero la kapolo wanu ndi pembedzero la anthu anu Aisrayeli, kuwamveram'menemonseakapfuula kwa Inu.