1 Kings 8:54 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Solomoni atamaliza kupemphera mopemba kwa Chauta, adadzuka ku guwa la Chauta kumene anali atagwada, manja atakweza kumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali kuti atatsiriza Solomoni kupemphera kwa Yehova pemphero ndi pembedzero lino lonse, ananyamuka ku guwa la nsembe la Yehova pomwe analikugwada pa mabondo ake, ndi manja ake otambasulira kumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Solomoni atamaliza mapemphero ndi mapembedzero onsewa kwa Yehova, anayimirira pa guwa lansembe la Yehova, nagwada atakweza manja ake kumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali kuti atatsiriza Solomo kupemphera kwa Yehova pemphero ndi pembedzero lino lonse, ananyamuka ku guwa la nsembe la Yehova pomwe analikugwada pa mabondo ace, ndi manja ace otambasulira kumwamba.