1 Kings 8:58 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atembenuzire mitima yathu kwa Iye, kuti tiziyenda m'njira zake ndi kusunga mau ake, malamulo ake ndi malangizo ake, amene adapatsa makolo athu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti atitembenuzire kwa Iye yekha mitima yathu iyende m'njira zake zonse, ndi kusunga malamulo ake onse ndi malemba ake ndi maweruzo ake, amene anawalamulira makolo athu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atembenuzire mitima yathu kwa Iye, kuti tiyende mʼnjira zake zonse ndi kusunga mawu ake, malamulo ake ndi malangizo ake amene anapereka kwa makolo athu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti atitembenuzire kwa iye yekha mitima yathu iyende m'njira zace zonse, ndi kusunga malamulo ace onse ndi malemba ace ndi maweruzo ace, amene anawalamulira makolo athu.