1 Kings 9:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Solomoni atamaliza kumanga Nyumba ya Chauta ndi nyumba ya mfumu, ndiponso zonse zimene iye ankafuna kuti amange,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, atasiriza Solomoni kumanga nyumba ya Yehova, ndi nyumba ya mfumu, ndi chifuniro chonse cha Solomoni anachikhumbacho,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Solomoni atatsiriza kumanga Nyumba ya Yehova ndi nyumba yaufumu, ndi kukwaniritsa kuchita zonse zimene ankafuna,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, atatsiriza Solomo kumanga nyumba ya Yehova, ndi nyumba ya mfumu, ndi cifuniro conse ca Solomo anacikhumbaco,