1 Kings 9:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake adafunsa kuti, “Kodi iwe mbale wanga, monga ndi imeneyi mizinda imene wandipatsa?” Choncho imatchulidwa kuti dziko la Kabule mpaka lero lino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati, Midzi yino mwandipatsayi njotani, mbale wanga? Naitcha dzina lao, Dziko lachikole, kufikira lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anafunsa kuti, “Mʼbale wanga, kodi iyi nʼkukhala mizinda yondipatsa?” Ndipo iye anayitcha mizindayo Dziko la Kabuli, dzina lomwe amatchedwa mpaka lero lino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati, Midzi yino mwandipatsayi njotani, mbale wanga? Naicha dzina lao, Dziko lacikole, kufikira lero lino.