1 Kings 9:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Izi ndizo zimene adachita mfumu Solomoni: adalamula anthu kuti agwire ntchito yathangata pomanga Nyumba ya Chauta, nyumba yake, linga lotchedwa Milo kudzanso khoma lozinga Yerusalemu, ndiponso mizinda ya Hazori, Megido ndi Gezere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chifukwa chake cha msonkho uja anausonkhetsa mfumu Solomoni ndi chimenechi; kuti amange nyumba ya Yehova, ndi nyumba ya iye yekha, ndi Milo, ndi linga la Yerusalemu, ndi Hazori, ndi Megido, ndi Gezere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Izi ndi zimene anachita Mfumu Solomoni: Analamula anthu kuti agwire ntchito yathangata pomanga Nyumba ya Yehova, nyumba yake, malo achitetezo a Milo, mpanda wa Yerusalemu, Hazori, Megido ndi Gezeri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cifukwa cace ca msonkho uja anausonkhetsa mfumu Solomo ndi cimeneci; kuti amange nyumba ya Yehova, ndi nyumba ya iye yekha, ndi Milo, ndi linga la Yerusalemu, ndi Hazori, ndi Megido; ndi Gezeri.