1 Kings 9:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma analipo anthu ena otsalira a mitundu yosiyanasiyana: Aamori, Ahiti, Aperizi, Ahivi ndi Ayebusi. Ameneŵa sanali Aisraele,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Aamori, ndi Ahiti, ndi Aperizi, ndi Ahivi, ndi Ayebusi otsala, amene sanali a ana a Israele,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Panali anthu amene anatsala pakati pa mitundu ya Aamori, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi (anthu awa sanali Aisraeli).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Aamori, ndi Ahiti, ndi Aperizi, ndi Ahivi, ndi Ayebusi otsala, amene sanali a ana a Israyeli,