1 Kings 9:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumu Solomoni adapanga zombo zambiri ku Eziyoni-Gebere pafupi ndi Elati, pa gombe la Nyanja Yofiira, ku dziko la Edomu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu Solomoni anamanga zombo zambiri ku Eziyoni-Gebere uli pafupi ndi Eloti, m'mphepete mwa Nyanja Yofiira, ku dziko la Edomu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu Solomoni anapanganso sitima zapamadzi ku Ezioni Geberi, malo amene ali pafupi ndi Eloti ku Edomu, mʼmbali mwa Nyanja Yofiira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu Solomo anamanga zombo zambiri ku Ezioni Geberi uli pafupi ndi Eloti, pambali pa Nyanja Yofiira, ku dziko la Edomu.