1 Kings 9:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono amalinyerowo adapita ku Ofiri, ndipo adakatengako golide wokwanira makilogramu 14,000, nabwera naye kwa mfumu Solomoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo anafika ku Ofiri, natengako golide matalente mazana anai mphambu makumi awiri, nafika naye kwa mfumu Solomoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapita ku Ofiri ndipo anakatenga golide okwana makilogalamu 14,000, amene anamupereka kwa Mfumu Solomoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo anafika ku Ofiri, natengako golidi matalenti mazana anai mphambu makumi awiri, nafika naye kwa mfumu Solomo.