1 Kings 9:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma iwe ndi ana ako mukapatuka ndi kuleka kunditsata Ine, mukasiya malangizo ndi malamulo anga amene ndidakupatsani, nkuyamba kutumikira milungu ina ndi kumaipembedza,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mukadzabwerera pang'ono pokha osanditsata, kapena inu, kapena ana anu, osasunga malamulo anga ndi malemba anga amene ndawaika pamaso panu; mukadzatumikira milungu ina ndi kuilambira;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma ngati iwe kapena ana ako mudzapatuka ndi kuleka kusunga malamulo ndi mawu anga amene ndakupatsani ndi kupita kukatumikira milungu ina ndi kuyipembedza,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mukadzabwerera pang'ono pokha osanditsata, kapena inu, kapena ana anu, osasunga malamulo anga ndi malemba anga amene ndawaika pamaso panu; mukadzatumikira milungu yina ndi kuilambira;