1 Peter 1:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja mau a Mulungu amanena kuti, “Anthu onse ali ngati udzu, ulemerero wao uli ngati duŵa lakuthengo. Udzu umauma, ndipo duŵa limathothoka,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza, Anthu onse akunga udzu, ndi ulemerero wao wonse ngati duwa la udzu. Udzuwo ungofota, ndi duwa lake lingogwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti, “Anthu onse ali ngati udzu, ndipo ulemerero wawo uli ngati duwa la kuthengo. Udzu umafota ndipo duwa limathothoka,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza, 8 Anthu onse akunga udzu, Ndi ulemerero waowonse ngad duwa la udzu. Udzuwo ungotota, ndi duwa lace lingogwa;