1 Peter 1:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
koma mau a Ambuye ngokhala mpaka muyaya.” Mau ameneŵa ndi Uthenga Wabwino umene walalikidwa kwa inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma Mau a Mulungu akhala chikhalire. Ndipo mau olalikidwa kwa inu ndi awo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma mawu a Ambuye adzakhala mpaka muyaya.” Ndipo awa ndi mawu amene tinalalikira kwa inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
9 Koma Mau a Mulungu akhala cikhalire. Ndipo 10 mau olalikidwa kwa Inu ndi jawo.