1 Peter 2:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja m'Malembo mudalembedwa kuti. “Ndasankha mwala wamtengowapatali. Ndikuuika tsopano m'Ziyoni, ngati mwala wapangodya. Wokhulupirira Iye sadzachita manyazi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa kwalembedwa m'lembo, Taona, ndiika m'Ziyoni mwala wotsiriza wa pangodya, wosankhika, wa mtengo wake; ndipo wokhulupirira Iye sadzanyazitsidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti mʼMalemba mwalembedwa kuti, “Taonani, ndikuyika mwala wa maziko mu Ziyoni, wosankhika ndi wamtengowapatali. Amene akhulupirira Iye sadzachititsidwa manyazi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa kwalembedwa m'lembo, Taona, ndiika m'Ziyoni mwala wotsiriza wa pangondya, wosankhika, wa mtengo wace; Ndipo wokhulupirira iye sadzanyazitsidwa.