1 Peter 2:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mau a Mulungu akutinso, “Umenewu ndi mwala wokhumudwitsa anthu, ndi thanthwe loŵagwetsa.” Amakhumudwa popeza kuti amakana kumvera mau a Mulungu, ndipo anali oyeneradi kuti adzaone zotere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo, Mwala wakukhumudwa nao, ndi thanthwe lophunthwitsa. Kwa iwo akukhumudwa ndi mau, pokhala osamvera, kumenekonso adaikidwako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi “Mwala wopunthwitsa anthu ndiponso thanthwe limene limagwetsa anthu.” Iwo amapunthwa chifukwa samvera uthenga, pakuti ichi ndiye chinali chifuniro cha Mulungu pa iwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo, Mwala wakukhumudwa nao, ndi thanthwe lopunthwitsa; kwa iwo akukhumudwa ndi mau, pokhala osamvera, kumenekonso adaikidwako.