1 Peter 3:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja mau a Mulungu akuti. “Yemwe afuna kukondwera ndi moyo, ndi kuwona masiku abwino, aletse lilime lake kulankhula zoipa, ndiponso milomo yake kunena mabodza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti, Iye wofuna kukonda moyo, ndi kuona masiku abwino, aletse lilime lake lisanene choipa, ndi milomo yake isalankhule chinyengo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti, “Iye amene angakonde moyo ndi kuona masiku abwino, aletse lilime lake kuyankhula zoyipa, ndiponso milomo yake kunena mabodza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti, iye wofuna kukonda moyo, Ndi kuona masiku abwino, Aletse lilime lace lisanene coipa, Ndi milomo yace isalankhule cinyengo;