1 Peter 3:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndani angakuchiteni choipa ngati muchita changu pa zabwino?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndani iye amene adzakuchitirani choipa, ngati muchita nacho changu chinthu chabwino?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndani angakuchitireni zoyipa ngati muchita changu kuchita zabwino?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndani iye amene adzakucitirani coipa, ngati mucita naco cangu cinthu cabwino?