1 Peter 3:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngakhale mumve zoŵaŵa chifukwa cha chilungamo, mudzakhala odala ndithu. Musachite mantha ndi anthu, kapena kuvutika mu mtima,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Komatu ngatinso mukumva zowawa chifukwa cha chilungamo, odala inu; ndipo musaope pakuwaopa iwo, kapena musadere nkhawa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngakhale mumve zowawa chifukwa cha chilungamo, ndinu odala. “Musaope anthu, musachite mantha.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Komatu ngatinso mukamva zowawa cifukwa ca cilungamo, odala inu; ndipo musaope pakuwaopa iwo, kapena musadere nkhawa;