1 Peter 3:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nkwabwino kumva zoŵaŵa chifukwa chochita zabwino, ngati Mulungu wafuna choncho, koposa kumva zoŵaŵa chifukwa chochita zoipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti, kumva zowawa chifukwa cha kuchita zabwino, ndi kumva zowawa chifukwa cha kuchita zoipa, nkwabwino kumva zowawa chifukwa cha kuchita zabwino, ngati chitero chifuniro cha Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼkwabwino ngati ndi chifuniro cha Mulungu kumva zowawa chifukwa chochita zabwino kusiyana ndi kumva zowawa chifukwa chochita zoyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti, kumva zowawa cifukwa ca kucita zabwino, ndi kumva zowawa cifukwa ca kucita zoipa, nkwabwino kumva zowawa cifukwa ca kucita zabwino, ngati citero cifuniro ca Mulungu,