1 Peter 3:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sara yemwe ankamvera Abrahamu, ndi kumutcha “Mbuyanga.” Motero inu azimai, ndinu ana ake a Sarayo, ngati muchita bwino, osalola kuwopsedwa ndi kanthu kalikonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
monga Sara anamvera Abrahamu, namutcha iye mbuye; ameneyo mukhala ana ake ngati muchita bwino, osaopa choopsa chilichonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
monga Sara, amene anamvera Abrahamu namutcha iye mbuye wake. Akazi inu ndinu ana ake ngati muchita zoyenera, ndipo musaope choopsa chilichonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
monga Sara anamvera Abrahamu, namucha iye mbuye; ameneyo mukhala ana ace ngati mucita bwino, osaopa coopsa ciri conse.