1 Peter 4:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati mumva zoŵaŵa chifukwa chakuti ndinu akhristu, musachite manyazi, koma mulemekeze Mulungu chifukwa cha dzinalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma akamva zowawa ngati mkhristu asachite manyazi; koma alemekeze Mulungu m'dzina ili.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma ngati mumva zowawa chifukwa ndinu Mkhristu, musachite manyazi, koma muyamike Mulungu chifukwa cha dzinalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma akamva zowawa ngati Mkristu asacite manyazi; koma alemekeze Mulungu m'dzina ili.