1 Peter 4:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma iwo adzayenera kufotokoza okha mlandu wao kwa Mulungu amene ali wokonzeka kuweruza amoyo ndi akufa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amenewo adzamwerengera Iye wokhala wokonzeka kuweruza amoyo ndi akufa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma adzafotokoza okha mlandu wawo kwa Mulungu amene wakonzeka kuweruza amoyo ndi akufa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amenewo adzamwerengera iye wokhala wokonzeka kuweruza amoyo ndi akufa.