1 Peter 5:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anzanu a mu mpingo wa ku Babiloni akuti moni. Marko, mwana wanga, nayenso akuti moni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye wa ku Babiloni wosankhidwa pamodzi nanu akulankhulani; ateronso Marko mwana wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imani mwamphamvu mʼchisomochi. Mlongo wanu amene ali ku Babuloni, wosankhidwa pamodzi nanu akupereka moni, nayenso Marko, mwana wanga, akupereka moni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye wa ku Babulo wosankhidwa pamodzi nanu akulankhulani; ateronso Marko mwana wanga.