1 Peter 5:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musakhale ngati mafumu odzikuza potsogolera anthu amene muyenera kuŵayang'anira, koma onetsani chitsanzo chabwino kwa nkhosazo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
osati monga ochita ufumu pa iwo a udindo wanu, koma okhala zitsanzo za gululo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musakhale ngati mafumu pa amene mukuwayangʼanira, koma mukhale chitsanzo kwa gululo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
osati monga ocita ufumu pa iwo a udindo wanu, koma okhala zitsanzo za gululo.