1 Peter 5:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tulani pa Iye nkhaŵa zanu zonse, popeza kuti Iye ndiye amakusamalirani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kutaya pa Iye nkhawa yanu yonse, pakuti Iye asamalira inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tayani pa Iye nkhawa zanu zonse chifukwa ndiye amakusamalani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kutaya pa iye nkhawa yanu yonse, pakuti iye asamalira inu.