1 Samuel 10:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Saulo nayenso adapita kwao ku Gibea, ndipo adatsakana naye anthu amphamvu amene Mulungu adaŵafeŵetsa mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Saulo yemwe anamuka kunyumba yake ku Gibea; ndipo am'khamu anatsagana naye iwo amene Mulungu adakhudza mitima yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sauli anapitanso ku mudzi kwawo ku Gibeya, pamodzi ndi anthu amphamvu amene Mulungu anawafewetsa mitima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Sauli yemwe anamuka ku nyumba yace ku Gibeya; ndipo am'khamu anatsagana naye iwo amene Mulungu adakhudza mitima yao.